OG Issah joins Zomba Changalume parliamentary by-elections
A popular Blantyre-based businessman OG Issah has joined the Zomba Changalume parliamentary race.
Mahomed Hanif Osman popularly known as ‘OG Issa’ is upbeat that he will win yhe parliamentary seat.
Reports say Osman will stand as an independent candidate and will contest with other candidates standing on PP, UTM, DPP and UDF tickets.
Osman was 2014-2019 legislator for Chiradzulu Central Constituency.
Malawi Congress Party is not featuring any candidate but will support one of the candidates.
Zomba Changalume Parliamentary seat fell vacant after the death of legislator John Chikalimba who was also leader for PP in the National Assembly.
Follow and Subscribe Nyasa TV :
I hope he has not misused his position just to a aquire land in chiradzulu.
Palibe chomwe munatipangira Ku chiradzulu central kuno, musapeperetsenso ena boss
At least this one votes, not the “dziko ndi wanu ndalama ndi wathu” type. Komabe ndi m’Mwenye basi.
Racist
A ku zomba sife opusa atiuze kwawo
Wachika ku Chiradzulo kukaimira ku Zomba? Moti anthu aku changalume adzikavotera zopusa zimenezi kusiya mbadwa zakonko zoti zikawa thandiza? Anthu amenewa atijaila kobasi, ngakhale mumawa bakira kuti ndi akuno koma olo ntakakhala ku dziko la amwenye mdzukulu wanga sangaka imire u MP. Adya kokwana misonkho yathu
Koma amwenye atitola kwambiri angoyima kumene akufuna ali pheeee ndiye mmalawi okonda soya pieces atengeka naye basi nane ndikayime ku India koma
Palibe chimene anapanga ku CZ fans ya ku ZA musapusisike.
Wawina kale uyu
Kwawo ndi ku Chiladzulo kapena ku Zomba. Anene bwino ameneyu kapen ku Chilazulo ndi kwawo kwa amake.
Back in the day, we used to go and buy audio cassettes at OG Issa. He was one of the top guys selling audio cassettes and I am 47 now. I am sure a lot of people will remember those days.
…ndipo gulu limeneli la amwenye amakaseti ili linkabera achina Mlaka, Billy Kaunda, Master Tongole,…oyimba onseeee. Mwini luso kutchuka koma wokudya mane n’kukhala OG Issa, mwini luso kumangonyambitira fungo. Ndiye chifukwa chake Matafale anawatopera. Woyimba kufufuza pa ground kupeza kuti almost banja lililonse linagula kaseti ya Nsaku koma Nsaku mwiniwakeyo kulandirako zamakaseti 1000 basi, eeeeh OG Issa ayi ndithu. Ndichifukwa chake wathawano ku Chiradzulo atamuzindikira bodza lake kuti akabodzenso ku Zomba, mwinanso next time adzayimira ku Likoma. Kaya ku Zomba analembetsako bwanji kaya, m’mwenye woti anakhazikika ku Mzedi? Nayo MCP ilibe manyazi kumapangana naye zimenezi mwamseli. That is how desperate MCP… Read more »
..and how old is OGI if you are 47 now