Madonna ends Malawi visit after meeting father of adopted son
Madonna left Malawi on Monday after a visit that included meetings with the president and the biological father of one of her adopted children.
Sarah Ezzy, director of the U.S. pop star’s charity Raising Malawi, confirmed Madonna’s departure on her private jet.
Madonna has been visiting Malawi since 2006. She funds a number of orphanages and schools in the country. On Thursday, she helped open a new 50-bed pediatrics ward in the commercial capital, Blantyre, that she helped fund.
On this visit, Madonna met President Peter Mutharika as well as Yohane Banda, father of her adopted son, 9-year-old David Banda. Madonna has another Malawi-born child, Mercy Chifundo James.—Associated Press
zoona zikuoneka kuti abomawa sakuonetsa kuti mavutowa atha kuwasova. Maunduna ambiri ali ndi anthu oti sakudziwa chimene akuchita.
Kukaona ndi mtima wa munthu chabe otherwise its by force nkhalambazo sozimadziwa kuti adoption ndi chani amvetsetseni
Madona ndi nyatwa mumafuna mutakhala inu
what about relatives of mercy? you didnt meet them
masosalawo ndiye alibwinotu.
ali nawo mwai poti anapeza omuthandza kulera mwana
Prophet ndiwachimidzi
Prophet ndiwe mbuzidi chotukwanira mchiyani pamenepa umafuna uli iwe ukusilira mwana akukula bwino iwe wakalamba sangakutenge ufa usanatchuke komanso ndi umphawi kumangotukwana basi kulira ndi mtimatu kumeneko
Ndipo kukalamba kuli apo, mwnanso ndo gojo. Ngati anabeleka, ndekuti akuvutika kulela anawo.
Pastor,not that am jealous of anybody but just think a child being called an orphan and still his father is alive.
zomwezi mpaka ma unifomu, koma a mw ndi anthu ovetsa cisoni,
muone mmene atakatile anthu kusolola,
koma ndithu mulibe manya zi kudikila munthu wa 50 yrs kudzakumangilani skool akamafa nkugudumuka pa stage inu muli timangiledi, kunjaku mmene akutisekera anthu azungu? a plesident kugawa ndalama kumbali mwacisisi pomwe skool zathu ana akuphuzila pa ntengo ,modotha ,hhhee koma za ndondoli.
ntila ni anjimile anakamuka zaoyamba zija lelo muone chief civo , ps a maunduna akamukepo ,mudzandiuza.
wankulu akakhala kuipoa imamuuza ndi mphepo. mau aakulutu awa. APM …..
Mrs. Madonna Yohane Banda kkkkkkinkiest.A Yohah nkozo wanu ndithu.